Machitidwe 28:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Anali kuwalalikira za ufumu wa Mulungu ndi kuwaphunzitsa za Ambuye Yesu Khristu, mwaufulu wonse wa kulankhula+ popanda choletsa. Aroma 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zimenezi zidzaonekera pa tsiku limene Mulungu, kudzera mwa Khristu Yesu, adzaweruze+ zinthu zobisika+ za anthu,+ mogwirizana ndi uthenga wabwino umene ndikulengeza.+
31 Anali kuwalalikira za ufumu wa Mulungu ndi kuwaphunzitsa za Ambuye Yesu Khristu, mwaufulu wonse wa kulankhula+ popanda choletsa.
16 Zimenezi zidzaonekera pa tsiku limene Mulungu, kudzera mwa Khristu Yesu, adzaweruze+ zinthu zobisika+ za anthu,+ mogwirizana ndi uthenga wabwino umene ndikulengeza.+