Mateyu 5:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tangotsimikizani kuti mukati Inde akhaledi Inde, ndipo mukati Ayi akhaledi Ayi,+ pakuti mawu owonjezera pamenepa achokera kwa woipayo.+ 2 Akorinto 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano pamene ndinali ndi cholinga chimenechi, kodi ndinali kulingalira mwachibwana?+ Kapena kodi zimene ndimaganiza kuti ndichite, ndimaziganiza ndi zolinga zadyera,+ kuti ndikati “Inde, inde” nthawi yomweyo ndisinthe ndinene kuti “Ayi, ayi”?+ 1 Timoteyo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 adama,+ amuna ogonana ndi amuna anzawo, oba anthu, onama, olumbira monama,+ ndiponso ochita china chilichonse chosagwirizana+ ndi chiphunzitso cholondola.+
37 Tangotsimikizani kuti mukati Inde akhaledi Inde, ndipo mukati Ayi akhaledi Ayi,+ pakuti mawu owonjezera pamenepa achokera kwa woipayo.+
17 Tsopano pamene ndinali ndi cholinga chimenechi, kodi ndinali kulingalira mwachibwana?+ Kapena kodi zimene ndimaganiza kuti ndichite, ndimaziganiza ndi zolinga zadyera,+ kuti ndikati “Inde, inde” nthawi yomweyo ndisinthe ndinene kuti “Ayi, ayi”?+
10 adama,+ amuna ogonana ndi amuna anzawo, oba anthu, onama, olumbira monama,+ ndiponso ochita china chilichonse chosagwirizana+ ndi chiphunzitso cholondola.+