Yohane 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+ Aheberi 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma chakudya chotafuna ndi cha anthu okhwima mwauzimu, amene pogwiritsa ntchito mphamvu zawo za kuzindikira,+ aphunzitsa mphamvuzo kusiyanitsa choyenera ndi chosayenera.+
3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+
14 Koma chakudya chotafuna ndi cha anthu okhwima mwauzimu, amene pogwiritsa ntchito mphamvu zawo za kuzindikira,+ aphunzitsa mphamvuzo kusiyanitsa choyenera ndi chosayenera.+