1 Yohane 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma mawu alionse ouziridwa amene amatsutsa zoti Yesu anabwera monga munthu, amenewo si ochokera kwa Mulungu,+ ndipo ndi ouziridwa ndi wokana Khristu amene munamva kuti akubwera,+ ndipo tsopano ali kale m’dziko.+ 2 Yohane 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 popeza anthu onyenga ambiri alowa m’dziko,+ amene amatsutsa zakuti kalero Yesu Khristu anabwera monga munthu.+ Amene amachita zimenezi ndi wonyenga+ uja ndiponso wokana Khristu.+
3 Koma mawu alionse ouziridwa amene amatsutsa zoti Yesu anabwera monga munthu, amenewo si ochokera kwa Mulungu,+ ndipo ndi ouziridwa ndi wokana Khristu amene munamva kuti akubwera,+ ndipo tsopano ali kale m’dziko.+
7 popeza anthu onyenga ambiri alowa m’dziko,+ amene amatsutsa zakuti kalero Yesu Khristu anabwera monga munthu.+ Amene amachita zimenezi ndi wonyenga+ uja ndiponso wokana Khristu.+