21 Miyalayo uiike malinga ndi mayina a mafuko a ana a Isiraeli, malinga ndi mayina a mafuko awo 12.+ Miyalayo ikhale yolembedwa mogoba ngati mmene amagobera chidindo, mwala uliwonse ukhale ndi limodzi mwa mayina a mafuko 12.+
14 Miyalayo anaiika malinga ndi mayina a mafuko a ana a Isiraeli, ndipo inalipo 12, malinga ndi mayina awo. Mwala uliwonse analembapo mochita kugoba limodzi mwa mayina a mafuko 12, ngati mmene amagobera chidindo.+