Yohane 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa Mulungu anakonda kwambiri dziko moti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense womukhulupirira asawonongedwe koma akhale ndi moyo wosatha.+ Aroma 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Popeza sanaumire ngakhale Mwana wake koma anamupereka mʼmalo mwa ife tonse,+ angalephere bwanji kutipatsanso mokoma mtima zinthu zina zonse pamodzi ndi Mwana wakeyo? Aheberi 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa cha chikhulupiriro, pamene Abulahamu anayesedwa,+ zinali ngati wapereka kale Isaki nsembe. Choncho munthu amene analandira malonjezo mokondwerayu, anali wokonzeka kupereka nsembe mwana wake yemwe anali mmodzi yekha.+
16 Chifukwa Mulungu anakonda kwambiri dziko moti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense womukhulupirira asawonongedwe koma akhale ndi moyo wosatha.+
32 Popeza sanaumire ngakhale Mwana wake koma anamupereka mʼmalo mwa ife tonse,+ angalephere bwanji kutipatsanso mokoma mtima zinthu zina zonse pamodzi ndi Mwana wakeyo?
17 Chifukwa cha chikhulupiriro, pamene Abulahamu anayesedwa,+ zinali ngati wapereka kale Isaki nsembe. Choncho munthu amene analandira malonjezo mokondwerayu, anali wokonzeka kupereka nsembe mwana wake yemwe anali mmodzi yekha.+