Ekisodo 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwa ndi chala cha Mulungu.+ Ekisodo 40:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako anatenga Umboni+ ndi kuuika mu Likasa,+ ndipo analowetsa ndodo zonyamulira+ mʼmbali mwa Likasalo nʼkuika chivundikiro+ pamwamba pa Likasa.+ 1 Mafumu 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mu Likasalo munalibe chinthu china chilichonse kupatulapo miyala iwiri yosema+ imene Mose anaikamo+ ku Horebe. Anaiikamo pa nthawi imene Yehova anachita pangano+ ndi Aisiraeli, pamene ankachoka mʼdziko la Iguputo.+ Aheberi 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mmenemu munali chiwaya chagolide chofukizira nsembe+ ndi likasa la pangano+ lokutidwa ndi golide.+ Mulikasamo munali mtsuko wagolide wokhala ndi mana,+ ndodo ya Aroni imene inaphuka ija+ komanso miyala yosema+ ya pangano.
18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwa ndi chala cha Mulungu.+
20 Kenako anatenga Umboni+ ndi kuuika mu Likasa,+ ndipo analowetsa ndodo zonyamulira+ mʼmbali mwa Likasalo nʼkuika chivundikiro+ pamwamba pa Likasa.+
9 Mu Likasalo munalibe chinthu china chilichonse kupatulapo miyala iwiri yosema+ imene Mose anaikamo+ ku Horebe. Anaiikamo pa nthawi imene Yehova anachita pangano+ ndi Aisiraeli, pamene ankachoka mʼdziko la Iguputo.+
4 Mmenemu munali chiwaya chagolide chofukizira nsembe+ ndi likasa la pangano+ lokutidwa ndi golide.+ Mulikasamo munali mtsuko wagolide wokhala ndi mana,+ ndodo ya Aroni imene inaphuka ija+ komanso miyala yosema+ ya pangano.