Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 28:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Zovala zoti apange ndi izi: chovala pachifuwa,+ efodi,+ malaya akunja odula manja,+ mkanjo wamandalasi, nduwira+ ndi lamba wapamimba.+ Aroni mʼbale wako ndi ana ake awapangire zovala zopatulikazi, kuti atumikire monga ansembe anga.

  • Levitiko 8:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Atatero anaveka Aroni mkanjo+ nʼkumumanga lamba wapamimba.*+ Anamuvekanso malaya odula manja+ komanso efodi+ ndipo anamanga lamba woluka+ wa efodiyo.

  • Levitiko 16:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Azivala mkanjo wopatulika wansalu,+ kabudula wansalu+ wobisa* thupi lake, azimanga lamba wansalu wapamimba,+ ndipo azikulunga kumutu kwake ndi nduwira yansalu.+ Zimenezi ndi zovala zopatulika.+ Iye azivala zimenezi atasamba thupi lonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena