Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 34:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mose anamwalira ali ndi zaka 120.+ Pa nthawiyo maso ake ankaonabe bwinobwino ndipo anali adakali ndi mphamvu.

  • Yobu 42:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pambuyo pa zimenezi, Yobu anakhala ndi moyo zaka 140 ndipo anaona ana ake ndi zidzukulu zake mpaka mʼbadwo wa 4.

  • Salimo 103:3-5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Iye amakukhululukira zolakwa zako zonse+

      Ndipo amachiritsa matenda ako onse.+

       4 Iye amawombola moyo wako kudzenje,*+

      Ndipo amakuveka chikondi chake chokhulupirika komanso chifundo ngati chisoti chachifumu.+

       5 Iye amakupatsa zinthu zabwino+ nthawi yonse ya moyo wako, zimene umakhutira nazo,

      Kuti ukhalebe wachinyamata ndi wamphamvu ngati chiwombankhanga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena