Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Anthu ochokera mʼmitundu yosiyanasiyana adzabwera nʼkunena kuti:

      “Bwerani. Tiyeni tipite kukakwera phiri la Yehova,

      Tipite kunyumba ya Mulungu wa Yakobo.+

      Iye akatiphunzitsa njira zake,

      Ndipo ife tidzayenda mʼnjira zakezo.”+

      Chifukwa chilamulo chidzaphunzitsidwa* mu Ziyoni,

      Ndipo mawu a Yehova adzaphunzitsidwa mu Yerusalemu.+

  • Mika 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Anthu ochokera mʼmitundu yosiyanasiyana adzabwera nʼkunena kuti:

      “Bwerani, tiyeni tipite kuphiri la Yehova,

      Tipite kunyumba ya Mulungu wa Yakobo.+

      Iye akatiphunzitsa njira zake,

      Ndipo ife tidzayenda mʼnjira zakezo.”

      Chifukwa chilamulo,* chidzaphunzitsidwa mu Ziyoni

      Ndipo mawu a Yehova adzaphunzitsidwa mu Yerusalemu.

  • Zekariya 8:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Yehova wanena kuti, ‘Ndidzabwerera ku Ziyoni+ ndipo ndizidzakhala ku Yerusalemu.+ Yerusalemu adzatchedwa mzinda wa choonadi*+ ndipo phiri la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba lidzatchedwa phiri loyera.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena