Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 8:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Zeba ndi Zalimuna atayamba kuthawa, iye anawathamangitsa mpaka kuwagwira. Mafumu a Midiyaniwa atagwidwa, gulu lawo lonse linachita mantha.

  • Oweruza 8:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Choncho, Aisiraeli anagonjetsa Amidiyani,+ ndipo Amidiyaniwo anasiya kulimbana nawo.* Zitatero, dziko linakhala pa mtendere zaka 40 mʼmasiku a Gidiyoni.+

  • Yesaya 10:26, 27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzamʼkwapula ndi chikwapu+ ngati mmene anachitira pamene anagonjetsa Midiyani pathanthwe la Orebi.+ Adzatambasula ndodo yake ndi kuloza panyanja ndipo adzaikweza mʼmwamba ngati mmene anachitira ndi Iguputo.+

      27 Tsiku limenelo katundu wake adzachoka paphewa panu,+

      Ndipo goli lake lidzachoka mʼkhosi mwanu.+

      Golilo lidzathyoledwa+ chifukwa cha mafuta.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena