Yesaya 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye wapita kukachisi ndi ku Diboni,+Wapita kumalo okwezeka kukalira. Mowabu akulira mofuula chifukwa cha zimene zachitikira Nebo+ ndi Medeba.+ Mutu uliwonse aumeta mpala+ ndipo ndevu zonse zametedwa.+ Yeremiya 48:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mowabu wachititsidwa manyazi ndipo wagwidwa ndi mantha aakulu. Lirani mofuula. Lengezani ku Arinoni+ kuti Mowabu wawonongedwa.
2 Iye wapita kukachisi ndi ku Diboni,+Wapita kumalo okwezeka kukalira. Mowabu akulira mofuula chifukwa cha zimene zachitikira Nebo+ ndi Medeba.+ Mutu uliwonse aumeta mpala+ ndipo ndevu zonse zametedwa.+
20 Mowabu wachititsidwa manyazi ndipo wagwidwa ndi mantha aakulu. Lirani mofuula. Lengezani ku Arinoni+ kuti Mowabu wawonongedwa.