-
Ezekieli 40:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Atandilowetsa mʼbwalo lamkati kudzera kumʼmawa, anayeza kanyumba kapagetiko ndipo anapeza kuti miyezo yake ndi yofanana ndi ya tinyumba tina tija.
-
-
Ezekieli 40:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Khonde lake linayangʼana kubwalo lakunja ndipo pazipilala zake zamʼmbali panali zithunzi za mtengo wa kanjedza ndipo anthu akafuna kulowa mʼkanyumbako amakwera masitepe 8.
-
-
Ezekieli 40:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Zipilala zake zamʼmbali zinayangʼana kubwalo lakunja ndipo pazipilala zonsezo panali zithunzi za mtengo wa kanjedza. Anthu akafuna kulowa mʼkanyumbako amakwera masitepe 8.
-