Salimo 87:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 87 Maziko a mzinda wa Mulungu ali mʼmapiri opatulika.+ 2 Yehova amakonda kwambiri mageti a Ziyoni+Kuposa matenti onse a Yakobo. Zekariya 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova wanena kuti, ‘Ndidzabwerera ku Ziyoni+ ndipo ndizidzakhala ku Yerusalemu.+ Yerusalemu adzatchedwa mzinda wa choonadi*+ ndipo phiri la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba lidzatchedwa phiri loyera.’”+
87 Maziko a mzinda wa Mulungu ali mʼmapiri opatulika.+ 2 Yehova amakonda kwambiri mageti a Ziyoni+Kuposa matenti onse a Yakobo.
3 “Yehova wanena kuti, ‘Ndidzabwerera ku Ziyoni+ ndipo ndizidzakhala ku Yerusalemu.+ Yerusalemu adzatchedwa mzinda wa choonadi*+ ndipo phiri la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba lidzatchedwa phiri loyera.’”+