Chivumbulutso 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako ndinayangʼana ndipo ndinaona Mwanawankhosa+ ataimirira paphiri la Ziyoni.+ Iye anali limodzi ndi enanso 144,000+ amene analembedwa dzina lake ndi dzina la Atate+ wake pazipumi zawo. Chivumbulutso 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo ankaimba nyimbo imene inkamveka ngati nyimbo yatsopano+ pamaso pa mpando wachifumu, pamaso pa angelo 4+ ndi pamaso pa akulu.+ Palibe amene anatha kuphunzira nyimboyo kupatulapo 144,000+ amene anagulidwa padziko lapansi.
14 Kenako ndinayangʼana ndipo ndinaona Mwanawankhosa+ ataimirira paphiri la Ziyoni.+ Iye anali limodzi ndi enanso 144,000+ amene analembedwa dzina lake ndi dzina la Atate+ wake pazipumi zawo.
3 Iwo ankaimba nyimbo imene inkamveka ngati nyimbo yatsopano+ pamaso pa mpando wachifumu, pamaso pa angelo 4+ ndi pamaso pa akulu.+ Palibe amene anatha kuphunzira nyimboyo kupatulapo 144,000+ amene anagulidwa padziko lapansi.