YOHANE
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Mawu anakhala munthu (1-18)
Umboni umene Yohane Mʼbatizi anapereka (19-28)
Yesu ndi Mwanawankhosa wa Mulungu (29-34)
Ophunzira oyambirira a Yesu (35-42)
Filipo komanso Natanayeli (43-51)
2
Ukwati ku Kana; anasandutsa madzi kukhala vinyo (1-12)
Yesu anayeretsa kachisi (13-22)
Yesu amadziwa zimene zili mumtima mwa munthu (23-25)
3
4
Yesu ndi mayi wa ku Samariya (1-38)
Asamariya ambiri anakhulupirira Yesu (39-42)
Yesu anachiritsa mwana wamwamuna wa mtumiki wa mfumu (43-54)
5
Munthu wodwala anachiritsidwa ku Betizata (1-18)
Yesu anapatsidwa ulamuliro ndi Atate wake (19-24)
Akufa adzamva mawu a Yesu (25-30)
Maumboni okhudza Yesu (31-47)
6
Yesu anadyetsa anthu 5,000 (1-15)
Yesu anayenda pamadzi (16-21)
Yesu ndi “chakudya chopatsa moyo” (22-59)
Ambiri anakhumudwa ndi mawu a Yesu (60-71)
7
Yesu anapita ku Chikondwerero cha Misasa (1-13)
Yesu anaphunzitsa kuchikondwerero (14-24)
Anthu anali ndi maganizo osiyanasiyana okhudza Khristu (25-52)
8
9
Yesu anachiritsa munthu amene anabadwa wosaona (1-12)
Munthu amene anachiritsidwa anafunsidwa mafunso ndi Afarisi (13-34)
Afarisi anali osaona (35-41)
10
Mʼbusa ndi makola a nkhosa (1-21)
Ayuda anakumana ndi Yesu ku Chikondwerero Chopereka Kachisi kwa Mulungu (22-39)
Ayuda ambiri anakana kukhulupirira (24-26)
“Nkhosa zanga zimamva mawu anga” (27)
Mwana ndi wogwirizana ndi Atate (30, 38)
Anthu ambiri akutsidya la Yorodano anakhulupirira (40-42)
11
Imfa ya Lazaro (1-16)
Yesu anatonthoza Marita ndi Mariya (17-37)
Yesu anaukitsa Lazaro (38-44)
Chiwembu choti aphe Yesu (45-57)
12
Mariya anathira mafuta pamapazi a Yesu (1-11)
Yesu analowa mumzinda mwaulemerero (12-19)
Yesu ananeneratu za imfa yake (20-37)
Kupanda chikhulupiriro kwa Ayuda kunakwaniritsa ulosi (38-43)
Yesu anabwera kudzapulumutsa dziko (44-50)
13
Yesu anasambitsa mapazi a ophunzira ake (1-20)
Yesu ananena kuti Yudasi adzamupereka (21-30)
Lamulo latsopano (31-35)
Ananeneratu kuti Petulo adzamukana (36-38)
14
15
Fanizo la mtengo wa mpesa weniweni (1-10)
Lamulo loti tizisonyeza chikondi ngati cha Khristu (11-17)
Dziko limadana ndi ophunzira a Yesu (18-27)
16
Ophunzira a Yesu akhoza kuphedwa (1-4a)
Ntchito ya mzimu woyera (4b-16)
Chisoni cha ophunzira chidzasanduka chisangalalo (17-24)
Yesu anagonjetsa dziko (25-33)
17
18
Yudasi anapereka Yesu (1-9)
Petulo anagwiritsa ntchito lupanga (10, 11)
Yesu anamupititsa kwa Anasi (12-14)
Petulo anakana Yesu koyamba (15-18)
Yesu anaonekera pamaso pa Anasi (19-24)
Petulo anakana Yesu kachiwiri ndi kachitatu (25-27)
Yesu anaonekera pamaso pa Pilato (28-40)
19
Yesu anakwapulidwa ndi kuchitiridwa zachipongwe (1-7)
Pilato anafunsanso Yesu (8-16a)
Yesu anamukhomerera pamtengo ku Gologota (16b-24)
Yesu anakonza zoti mayi ake asamaliridwe (25-27)
Imfa ya Yesu (28-37)
Kuikidwa mʼmanda kwa Yesu (38-42)
20
Manda opanda kanthu (1-10)
Yesu anaonekera kwa Mariya wa ku Magadala (11-18)
Yesu anaonekera kwa ophunzira ake (19-23)
Tomasi anakayikira koma kenako anakhulupirira (24-29)
Cholinga cha mpukutuwu (30, 31)
21
Yesu anaonekera kwa ophunzira ake (1-14)
Petulo anatsimikizira kuti amakonda Yesu (15-19)
Tsogolo la wophunzira wa Yesu amene ankamukonda kwambiri (20-23)
Mawu omaliza (24, 25)