MATEYU
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
2
Okhulupirira nyenyezi anapita kukamuona (1-12)
Anathawira ku Iguputo (13-15)
Herode anapha ana aamuna (16-18)
Anabwerera ku Nazareti (19-23)
3
4
Mdyerekezi anayesa Yesu (1-11)
Yesu anayamba kulalikira ku Galileya (12-17)
Anasankha ophunzira oyambirira (18-22)
Yesu ankalalikira, kuphunzitsa komanso kuchiritsa (23-25)
5
ULALIKI WAPAPHIRI (1-48)
Yesu anayamba kuphunzitsa paphiri (1, 2)
Zinthu 9 zimene zimapangitsa anthu kuti azikhala osangalala (3-12)
Mchere komanso kuwala (13-16)
Yesu anakwaniritsa Chilamulo (17-20)
Malangizo okhudza mkwiyo (21-26), chigololo (27-30), kutha kwa ukwati (31, 32), malumbiro (33-37), kubwezera (38-42), kukonda adani athu (43-48)
6
ULALIKI WAPAPHIRI (1-34)
Muzipewa kudzionetsera kuti ndinu olungama (1-4)
Mmene tingapempherere (5-15)
Kusala kudya (16-18)
Chuma padziko lapansi komanso kumwamba (19-24)
Siyani kuda nkhawa (25-34)
7
8
Anachiritsa munthu wakhate (1-4)
Chikhulupiriro cha mtsogoleri wa asilikali (5-13)
Yesu anachiritsa anthu ambiri ku Kaperenao (14-17)
Zimene tingachite kuti tizitsatira Yesu (18-22)
Yesu analetsa mphepo yamphamvu (23-27)
Yesu anatumiza ziwanda munkhumba (28-34)
9
Yesu anachiritsa munthu wakufa ziwalo (1-8)
Yesu anaitana Mateyu (9-13)
Funso lokhudza kusala kudya (14-17)
Mwana wamkazi wa Yairo; mzimayi anagwira chovala chakunja cha Yesu (18-26)
Yesu anachiritsa munthu wosaona komanso wosalankhula (27-34)
Zokolola nʼzochuluka, koma antchito ndi ochepa (35-38)
10
Atumwi 12 (1-4)
Malangizo okhudza kulalikira (5-15)
Ophunzira adzazunzidwa (16-25)
Muziopa Mulungu, osati anthu (26-31)
Osati mtendere, koma lupanga (32-39)
Kulandira ophunzira a Yesu (40-42)
11
Yohane Mʼbatizi analemekezedwa (1-15)
Anadzudzula mʼbadwo wosamvera (16-24)
Yesu anatamanda Atate wake chifukwa chokomera mtima anthu wamba (25-27)
Goli la Yesu limatsitsimula (28-30)
12
Yesu ndi “Mbuye wa Sabata” (1-8)
Anachiritsa munthu wolumala dzanja (9-14)
Mtumiki amene Mulungu amamukonda (15-21)
Anatulutsa ziwanda pogwiritsa ntchito mzimu woyera (22-30)
Tchimo losakhululukidwa (31, 32)
Mtengo umadziwika ndi zipatso zake (33-37)
Chizindikiro cha Yona (38-42)
Mzimu wonyansa ukabwerera (43-45)
Amayi ake a Yesu komanso azichimwene ake (46-50)
13
14
Yohane Mʼbatizi anadulidwa mutu (1-12)
Yesu anadyetsa anthu 5,000 (13-21)
Yesu anayenda pamadzi (22-33)
Anachiritsa anthu ku Genesareti (34-36)
15
Anadzudzula miyambo ya makolo (1-9)
Zodetsa zimachokera mumtima (10-20)
Chikhulupiriro cholimba cha mayi wa ku Foinike (21-28)
Yesu anachiritsa matenda ambiri (29-31)
Yesu anadyetsa anthu 4,000 (32-39)
16
Kupempha chizindikiro (1-4)
Zofufumitsa za Afarisi ndi Asaduki (5-12)
Makiyi a Ufumu (13-20)
Ananeneratu zokhudza imfa ya Yesu (21-23)
Chizindikiro cha ophunzira enieni (24-28)
17
Yesu anasintha maonekedwe (1-13)
Chikhulupiriro chofanana ndi kanjere ka mpiru (14-21)
Yesu ananeneratunso zokhudza imfa yake (22, 23)
Anapereka msonkho pogwiritsa ntchito ndalama yamkamwa mwa nsomba (24-27)
18
Wamkulu kwambiri mu Ufumu (1-6)
Zopunthwitsa (7-11)
Fanizo la nkhosa yosochera (12-14)
Zimene tingachite kuti tibweze mʼbale wathu (15-20)
Fanizo la kapolo wosakhululuka (21-35)
19
Ukwati komanso kutha kwa banja (1-9)
Mphatso ya kusakwatira (10-12)
Yesu anadalitsa ana (13-15)
Funso limene wachinyamata wolemera anafunsa (16-24)
Zinthu zimene tiyenera kudzimana chifukwa cha Ufumu (25-30)
20
Anthu amene ankagwira ntchito mʼmunda wampesa analandira malipiro ofanana (1-16)
Yesu ananeneratunso zokhudza imfa yake (17-19)
Anapempha kuti adzapatsidwe malo apadera mu Ufumu (20-28)
Amuna awiri osaona anachiritsidwa (29-34)
21
Yesu analowa mumzinda mwaulemerero (1-11)
Yesu anayeretsa kachisi (12-17)
Anatemberera mtengo wa mkuyu (18-22)
Anakayikira ulamuliro wa Yesu (23-27)
Fanizo la ana awiri aamuna (28-32)
Fanizo la alimi amene anapha anthu (33-46)
22
Fanizo la phwando laukwati (1-14)
Mulungu komanso Kaisara (15-22)
Funso lokhudza kuukitsidwa kwa akufa (23-33)
Malamulo awiri akuluakulu (34-40)
Kodi Khristu ndi mwana wa Davide? (41-46)
23
Musamatsanzire alembi ndi Afarisi (1-12)
Tsoka kwa alembi ndi Afarisi (13-36)
Yesu analirira Yerusalemu (37-39)
24
25
26
Ansembe anakonza chiwembu kuti aphe Yesu (1-5)
Yesu anathiridwa mafuta onunkhira (6-13)
Pasika womaliza komanso kuperekedwa (14-25)
Anayambitsa mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye (26-30)
Ananeneratu kuti Petulo adzamukana (31-35)
Yesu anapemphera ku Getsemane (36-46)
Yesu anagwidwa (47-56)
Anazengedwa mlandu ndi Khoti Lalikulu la Ayuda (57-68)
Petulo anakana Yesu (69-75)
27
Yesu anaperekedwa kwa Pilato (1, 2)
Yudasi anadzimangirira (3-10)
Yesu anaonekera kwa Pilato (11-26)
Anamuchitira zachipongwe pamaso pa anthu (27-31)
Anamukhomerera pamtengo ku Gologota (32-44)
Imfa ya Yesu (45-56)
Kuikidwa mʼmanda kwa Yesu (57-61)
Anakhwimitsa chitetezo pamanda ake (62-66)
28