MALIKO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Yohane Mʼbatizi ankalalikira (1-8)
Kubatizidwa kwa Yesu (9-11)
Yesu anayesedwa ndi Satana (12, 13)
Yesu anayamba kulalikira ku Galileya (14, 15)
Anasankha ophunzira oyambirira (16-20)
Anatulutsa mzimu wonyansa (21-28)
Yesu anachiritsa anthu ambiri ku Kaperenao (29-34)
Anapemphera kumalo opanda anthu (35-39)
Munthu wakhate anachiritsidwa (40-45)
2
Yesu anachiritsa munthu wakufa ziwalo (1-12)
Yesu anaitana Levi (13-17)
Funso lokhudza kusala kudya (18-22)
Yesu ndi ‘Mbuye wa Sabata’ (23-28)
3
Munthu wolumala dzanja anachiritsidwa (1-6)
Chigulu cha anthu chinali mʼmbali mwa nyanja (7-12)
Atumwi 12 (13-19)
Kunyoza mzimu woyera (20-30)
Mayi komanso azichimwene ake a Yesu (31-35)
4
5
6
Yesu anakanidwa mʼdera lakwawo (1-6)
Atumwi 12 anapatsidwa malangizo okhudza utumiki (7-13)
Imfa ya Yohane Mʼbatizi (14-29)
Yesu anadyetsa anthu 5,000 (30-44)
Yesu anayenda pamadzi (45-52)
Anachiritsa anthu ku Genesareti (53-56)
7
Anadzudzula miyambo ya anthu (1-13)
Zinthu zimene zimaipitsa munthu zimachokera mumtima (14-23)
Chikhulupiriro cha mayi wa Chisurofoinike (24-30)
Munthu amene anali ndi vuto losamva anachiritsidwa (31-37)
8
Yesu anadyetsa anthu 4,000 (1-9)
Anapempha chizindikiro (10-13)
Zofufumitsa za Afarisi ndi Herode (14-21)
Munthu wavuto losaona anachiritsidwa ku Betsaida (22-26)
Petulo anazindikira kuti Yesu ndi Khristu (27-30)
Yesu ananeneratu za imfa yake (31-33)
Chizindikiro cha wophunzira weniweni (34-38)
9
Yesu anasintha maonekedwe ake (1-13)
Mnyamata wogwidwa ndi chiwanda anachiritsidwa (14-29)
Yesu ananeneratu kachiwiri za imfa yake (30-32)
Ophunzira anakangana kuti wamkulu ndi ndani (33-37)
Aliyense amene sakulimbana nafe ali kumbali yathu (38-41)
Zopunthwitsa (42-48)
“Khalani ndi mchere mwa inu nokha” (49, 50)
10
Ukwati komanso kutha kwa banja (1-12)
Yesu anadalitsa ana (13-16)
Funso la munthu wachuma (17-25)
Zinthu zimene tikuyenera kudzimana chifukwa cha Ufumu (26-31)
Yesu ananeneratunso za imfa yake (32-34)
Pempho la Yakobo ndi Yohane (35-45)
Batimeyu amene anali ndi vuto losaona anachiritsidwa (46-52)
11
Yesu analowa mumzinda mwaulemerero (1-11)
Anatemberera mtengo wamkuyu (12-14)
Yesu anayeretsa kachisi (15-18)
Zimene tikuphunzira pa mtengo wamkuyu umene unafota (19-26)
Anatsutsa ulamuliro wa Yesu (27-33)
12
Fanizo la alimi amene anapha anthu (1-12)
Mulungu komanso Kaisara (13-17)
Funso lokhudza kuuka kwa akufa (18-27)
Malamulo awiri aakulu kwambiri (28-34)
Kodi Khristu ndi mwana wa Davide? (35-37a)
Anawachenjeza kuti asamale ndi alembi (37b-40)
Timakobidi tiwiri ta mayi wamasiye wosauka (41-44)
13
14
Ansembe anakonza zoti aphe Yesu (1, 2)
Anathira Yesu mafuta onunkhira kwambiri (3-9)
Yudasi anapereka Yesu (10, 11)
Pasika womaliza (12-21)
Anayambitsa Mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye (22-26)
Ananeneratu zoti Petulo adzamukana (27-31)
Yesu anapemphera ku Getsemane (32-42)
Yesu anagwidwa (43-52)
Anaimbidwa mlandu Mʼkhoti Lalikulu la Ayuda (53-65)
Petulo anakana Yesu (66-72)
15
Yesu anakaonekera pamaso pa Pilato (1-15)
Ananyozedwa pagulu (16-20)
Anamukhomerera pamtengo ku Gologota (21-32)
Imfa ya Yesu (33-41)
Kuikidwa mʼmanda kwa Yesu (42-47)
16