Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 11/09 tsamba 28-31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
  • Galamukani!—2009
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Chithunzichi Chalakwika Pati?
  • Zithunzi Zoti Ana Apeze
  • Kuchokera M’magazini Ino
  • Kodi Mumadziwa Chiyani za Woweruza Yefita?
  • MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
Onani Zambiri
Galamukani!—2009
g 11/09 tsamba 28-31

Kodi Mungayankhe Bwanji?

Kodi Chithunzichi Chalakwika Pati?

Werengani Machitidwe 8:26-40. Ndiyeno yang’anani pa chithunzipa. Kodi chalakwika pati? Lembani mayankho anu pa mizere ili m’munsiyi.

1. ․․․․․

2. ․․․․․

3. ․․․․․

KAMBIRANANI:

Kodi mdindoyo sankamvetsa zimene ankawerenga chifukwa chiyani? Kodi anathandizidwa bwanji kuti amvetse zimene ankawerenga? Kodi inuyo mungatsanzire bwanji mdindoyo?

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungathe kupeza zithunzi izi m’magazini ino? Fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

Kuchokera M’magazini Ino

Yankhani mafunsowa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo omwe akusowapo.

TSAMBA 8 Kodi muyenera ‘kuwombola’ chiyani? Aefeso 5:․․․

TSAMBA 9 Kodi tiyenera kuchenjera ndi chiyani? Luka 12:․․․

TSAMBA 10 Ngati mdani wanu ali ndi njala, kodi muyenera kumupatsa chiyani? Aroma 12:․․․

TSAMBA 20 Pankhani ya maonekedwe athu, kodi tiyenera kuganizira kwambiri za chiyani? 1 Petulo 3:․․․

Kodi Mumadziwa Chiyani za Woweruza Yefita?

Werengani Oweruza 11:1–12:7. Ndiyeno yankhani mafunso otsatirawa.

4. ․․․․․

Mwa mafuko 12 a Isiraeli, kodi iye anali wochokera m’fuko liti?

ZOKUTHANDIZANI: Werengani Numeri 26:29.

5. ․․․․․

Anapulumutsa Aisiraeli kuchokera kwa adani a mtundu uti?

6. ․․․․․

Zoona kapena Zonama? Iye anakhalapo Yosefe yemwe anali mwana wa Yakobo (Isiraeli), atafa.

KAMBIRANANI:

Kodi mukuganiza kuti mwana wa Yefita anavomera kuti bambo ake akwaniritse lumbiro lawo chifukwa chiyani? Kodi inuyo mungamutsanzire bwanji mwana wa Yefita?

◼ Mayankho ali pa tsamba 28

MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31

1. Filipo ayenera kuti anali yekha.

2. Mdindo anakwera galeta osati hatchi.

3. Izi zinachitikira m’chipululu, osati m’tauni momwe munali anthu ambiri.

4. Manase.—Numeri 26:29; Oweruza 11:1.

5. Amoni. Oweruza 11:4.

6. Zoona.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena