Thanzi
Zimene Baibulo Limanena: Thanzi Lathu Galamukani!, 4/2013
Madokotala Amakumana N’zambiri
Kodi Udokotala Uli ndi Tsogolo Lotani?
Chifukwa Chake Anthufe Timadwala Mphunzitsi Waluso, mutu 23
Thupi la Munthu
Tinapangidwa Modabwitsa’ Galamukani!, 5/2011
N’zotheka Ndithu Kuchepetsa Vuto la Kuiwala Galamukani!, 2/2009
‘Tinapangidwa Modabwitsa’ Nsanja ya Olonda, 6/15/2007
Kukongola ndi Kaonekedwe
Kodi Ndiyeneradi Kudandaula Ndi Mmene Ndimaonekera? Mayankho a Mafunso 10, funso 2
Zimene Baibulo Limanena: Kukongola Galamukani!, Na. 4 2016
Nkhawa Imene Munthu Ali Nayo pa Maonekedwe Ake Ikasanduka Matenda Galamukani!, 8/8/2004
Ziwalo za Thupi ndi Mmene Zimagwirira Ntchito
Misozi Yathu Ndi Yodabwitsa Kwambiri Galamukani!, 3/2014
Muziyamikira Mphatso Zimene Muli Nazo Galamukani!, 5/2011
Kodi Mungadziwe Bwanji Kuti Muli ndi Matenda a Chithokomiro? Galamukani!, 5/2009
Dzitetezeni Kuti Musagonthe M’kutu! Galamukani!, 6/8/2002
Kukhala ndi Thanzi Labwino
Zimene Mungachite Kuti Mukhale ndi Moyo Wathanzi Galamukani!, 6/2015
Kamphepo Kayaziyazi Komanso Dzuwa Ndi Mankhwala Galamukani!, 3/2015
3—Muzichita Masewera Olimbitsa Thupi
5—Muzikhala Wokonzeka Kusintha
Chitani Zinthu Zokuthandizani Kukhala ndi Thanzi Labwino
N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kusamalira Thanzi Langa? Achinyamata Amafunsa, Buku Loyamba, mutu 10
Kodi Pali Vuto Lililonse ndi Kukhalitsa Padzuwa? Galamukani!, 6/2009
N’chifukwa Chiyani Muyenera Kumakaonana ndi Dokotala wa Mano? Galamukani!, 5/2007
Tetezani Khungu Lanu Galamukani!, 6/8/2005
Mmene Kukonda Zinthu Zauzimu Kumakhudzira Moyo Wanu Nsanja ya Olonda, 2/1/2004
Njira Zisanu ndi Imodzi Zosamalira Thanzi Lanu Galamukani!, 10/8/2003
Zimene Mumasankha Zimakhudza Thanzi Lanu Galamukani!, 9/8/2003
Ukhondo
N’zotheka Kuthana ndi Nsikidzi Galamukani!, 12/2012
Matenda Amene Anavuta Kwambiri M’zaka za M’ma 1800 Galamukani!, 10/2010
N’chifukwa Chiyani Ukhondo Uli Wofunika? Nsanja ya Olonda, 12/1/2008
Sopo ndi “Katemera Amene Mungadzipatse Nokha” Galamukani!, 12/8/2003
Kodi Ukhondo Umatanthauza Chiyani Makamaka?
Masewera Olimbitsa Thupi
Kodi Mumachita Mokwanira Zinthu Zolimbitsa Thupi?
Masewero a Yoga—Kodi Ndi Ongolimbitsa Thupi Chabe Kapena Pali Zinanso? Nsanja ya Olonda, 8/1/2002
Zakudya Zopatsa Thanzi
Kuthana ndi Vuto la Kunenepa Kwambiri Galamukani!, 10/2012
2. Muziyesetsa Kukhala Aukhondo
3. Muziphika Komanso Kusunga Chakudya Pamalo Abwino
4. Muzisamala Mukamadya Kulesitanti
Posachedwapa Aliyense Azidzadya Zakudya Zosamalidwa Bwino
Kodi Kusala Kudya Kumathandiza Munthu Kuyandikira kwa Mulungu? Nsanja ya Olonda, 4/1/2009
Kodi Pagona Vutoli Mpati, Nanga Kuipa Kwake N’kotani? Galamukani!, 3/8/2003
Chakudya Chopatsa Thanzi N’chosasowa Galamukani!, 5/8/2002
Kugona
Mmene Mungapezere Tulo Tokwanira
Kuzindikira Matenda Atulo Aakulu
Zimene Mungachite Kuti Muzigona Bwino
Kodi Kuvutika Ndi Tulo kwa Achinyamata Ndi Nkhani Yodetsa Nkhaŵa? Galamukani!, 8/8/2002
Zimene Mungachite Mukamapanikizika Maganizo
Kumwetulira Ndi Mphatso Yofunika Kugawana Galamukani!, Na. 1 2017
Kodi Mungatani Ngati Mukuvutika Maganizo? Galamukani!, 5/2014
Kupanikizika Kumayambitsa Mavuto Aakulu
Zimene Tingachite Kuti Tisamapanikizike Kwambiri
Zimene Zimachititsa Moyo Kukhala Wopanikizika ndi Zotsatirapo Zake
Pali Zimene Mungachite Kuti Moyo Wanu Usakhale Wopanikizika
Mankhwala Omwe Angathandize Kuthetsa Nkhawa Nsanja ya Olonda, 12/15/2001
Thandizo Lachipatala
Sayansi Yamakono ya Zamankhwala—Kodi Ingafike Pati?
Thanzi Labwino kwa Onse—Lifika Posachedwapa!
Kusamalira Thanzi M’njira Yogwirizana ndi Malemba
Yehova Adzakuthandizani Pamene Mukudwala Nsanja ya Olonda, 12/15/2015
Pitirizani Kuyandikira Yehova (Kamutu: Thanzi) Nsanja ya Olonda, 1/15/2013
Samalirani Thanzi Lanu M’njira Yogwirizana ndi Malemba Nsanja ya Olonda, 11/15/2008
Njira Zina Zochizira Matenda
Muziganiza Bwino Kwambiri (Kamutu: Nkhani Zokhudza Umoyo) Nsanja ya Olonda, 3/1/2006
Kodi Mankhwala Ochokera ku Zitsamba Angakuthandizeni? Galamukani!, 1/8/2004
Zimene Baibulo Limanena: Kodi Akristu Azichita Zogodomalitsa Maganizo? Galamukani!, 7/8/2003
Kupenda Njira Zochiritsira Zosagwiritsidwa Ntchito Masiku Onse
Chosankha Chanu pa Chithandizo Chamankhwala
Matenda Ndiponso Mmene Thanzi la Munthu Lilili
Nkhanizi zikungofotokoza mfundo zosiyanasiyana zokhudza matenda osiyanasiyana ndipo cholinga chake sikupereka mankhwala kapena njira yochizira matenda. Munthu aliyense ayenera kuganiza mosamala asanapange chosankha pa nkhani ya thandizo lamankhwala, logwirizana ndi mfundo za m’Baibulo, limene akufuna kulandira.
Zambiri mwa nkhanizi ndi zochokera pa zimene anthu amene anakumana ndi vutolo ananena ndipo zingalimbikitse anthu ena amene akukumananso ndi vuto lomwelo.
Zimene Muyenera Kudziwa Zokhudza Matenda a Muubongo Galamukani!, 12/2014
Kodi Ndinalakwa Chiyani Kuti Ndidwale Chonchi? Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri, mutu 8
Zimene Mungachite Munthu Amene Mumakonda Akadwala Misala Galamukani!, 12/8/2004
Nkhondo Yakalekale Yofuna Kupeza Thanzi Labwino Galamukani!, 6/8/2004
Ziphuphu Pathupi la Munthu
‘Kodi Chikuchitika N’chiyani M’thupi Mwangamu?’ Galamukani!, 7/8/2004
Edzi
Zinthu Zolimbikitsa Zimene Zachitika pa Ntchito Yolimbana ndi Edzi
Ngati Mliri wa Edzi Udzagonjetsedwe, Kodi Ungadzagonjetsedwe Bwanji?
Ziwerengero Zochititsa Mantha za AIDS! Galamukani!, 3/8/2001
Amayi Odwala AIDS Akusowa Pogwira Galamukani!, 1/8/2000
Alubino
Vuto Lokhala Alubino Galamukani!, 7/2008
Matenda Obwera Chifukwa Chodana ndi Zinazake
Kodi Kudana ndi Kusagwirizana ndi Zakudya kwa Thupi N’kosiyana Bwanji? Galamukani!, Na. 3 2016
Matenda Otchedwa Alzheimer
“Mwina Nyimbo Ndi Imene Ingathandize” Galamukani!, 9/2010
Matenda Opha Ziwalo Otchedwa Amyotrophic Lateral Sclerosis (ALS)
Matendawa amatchedwanso matenda a Lou Gehrig
Chikhulupiriro Chandithandiza Kupirira Matenda Oopsa Galamukani!, 1/2006
Matenda a Kuda Nkhawa
Kodi Mungatani Kuti Muthandize Odwala Matenda Oda Nkhawa? Galamukani!, 3/2012
Kodi Vuto Lokhala Wamantha Mukamakumbukira Zoopsa Ndi Lotani Kwenikweni?
Nyamakazi
Kuwadziwa bwino Matenda a Nyamakazi
Odwala Nyamakazi Asataye Mtima
Matenda Otchedwa Asperger
Kulimbana ndi Matenda a Asperger Galamukani!, 9/2008
Khungu
Amachita Zinthu Bwinobwino Ngakhale Kuti Ndi Osaona Galamukani!, 11/2015
Baibulo Limasintha Anthu: Panopa Ndimaona Kuti Ndingathe Kuthandiza Ena Nsanja ya Olonda, 10/1/2015
“Ngati Kingsley Akukwanitsa, Kuli Bwanji Ine?” Nsanja ya Olonda, 6/15/2015
Muzithandiza Anthu Osaona Kudziwa za Yehova Utumiki wa Ufumu, 5/2015
Ndimakonda Nyimbo, Moyo, ndi Baibulo Galamukani!, 8/2007
Kodi Muli ndi Vuto Losiyanitsa Mitundu? Galamukani!, 7/2007
Ndinalandira ‘Zokhumba Mtima Wanga’ Nsanja ya Olonda, 11/1/2005
Maso Anga Anatseguka Ngakhale Kuti Ndinali Wakhungu! Nsanja ya Olonda, 5/1/2004
Matenda Otchedwa Body Dysmorphic Disorder (BDD)
Nkhawa Imene Munthu Ali Nayo pa Maonekedwe Ake Ikasanduka Matenda Galamukani!, 8/8/2004
Matenda Amene Anayamba ndi Makoswe (The Black Death)
Mliri wa Matenda a Makoswe—Unakantha Ulaya M’Nyengo Zapakati Galamukani!, 2/8/2000
Kupanikizika ndi Ntchito
Kodi Mungatani Ngati Mukupanikizika Chifukwa cha Ntchito? Galamukani!, 9/2014
Khansa
Zimene Mungachite Ngati Mwapezeka ndi Khansa ya M’mawere Galamukani!, 8/2011
Zimene Makolo Angachite Ngati Mwana Wawo Ali ndi Khansa Galamukani!, 5/2011
Kupirira ndi Khansa Yapakhungu
Matenda a Muubongo Olumalitsa Ziwalo (Cerebral Palsy)
Jairo Amagwiritsa Ntchito Maso Ake Kutumikira Mulungu Nsanja ya Olonda, 3/1/2015
Loida Ayamba Kulankhula Galamukani!, 5/8/2000
Matenda Ofanana ndi Kaodzera (Chagas’ Disease)
Matenda Ofalitsidwa ndi Tizilombo Akuvutitsa Kwambiri Galamukani!, 6/8/2003
Ntchofu
Ngati Mwana Wanu Wakhanda Sasiya Kulira Galamukani!, 5/8/2004
Matenda Otchedwa Cystic Fibrosis
Chikhulupiriro Chake Chimalimbikitsa Ena Nsanja ya Olonda, 7/1/2006
Kukhala Wogontha
Onani mutu wakuti Maphunziro ndi Chinenero ➤ Chinenero Chamanja
Matenda a Chingwangwa
Matenda a Chingwangwa Avuta Kwambiri Galamukani!, 11/2011
Matenda a Maganizo ndi Kuvutika Maganizo
N’chifukwa Chiyani Achinyamata Ambiri Akudwala Matenda Ovutika Maganizo? Galamukani!, Na. 1 2017
Zimene Muyenera Kudziwa Zokhudza Matenda a Muubongo Galamukani!, 12/2014
Zimene Baibulo Limanena: Kuvutika Maganizo Galamukani!, 10/2013
Yandikirani Mulungu: Nkhani Yolimbikitsa kwa Anthu Osweka Mtima Nsanja ya Olonda, 6/1/2011
❐ Galamukani!, 7/2009 Kodi Matenda Ovutika Maganizo Ndi Otani?
Kodi Mungathetse Bwanji Matenda Ovutika Maganizo?
“Mulungu wa Chitonthozo Chonse” Amathandiza
Musaope Yehova Ali Nanu Nsanja ya Olonda, 5/1/2006
Kukhala ndi Matenda a Maganizo
Nkhani Yabwino kwa Odwala Matendawa
“Simudziwa Chimene Chidzagwa Mawa” Nsanja ya Olonda, 12/1/2000
Matenda a Shuga
Zimene Mungachite Kuti Mupewe Matenda a Shuga Galamukani!, 9/2014
Mmene Baibulo Lingathandizire Odwala Matendawa
Kulumala
Ndilibe Manja Koma Ndinatha Kulandira Choonadi cha M’Baibulo Nsanja ya Olonda (Yogawira), Na. 6 2016
Kuthandiza Ana Amene Ali ndi Vuto Lophunzira Galamukani!, 1/2009
Kulera Ana Omwe Amafunika Kuwasamalira Mwapadera Galamukani!, 4/2006
Kukaona Malo Opangira Ziwalo Galamukani!, 2/2006
Kulumala N’kosiyanasiyana Nsanja ya Olonda, 5/1/2002
Matenda a Kuzerezeka
Kulera Ana Obadwa ndi Matenda Ozerezeka Galamukani!, 6/2011
Mavuto Amene Takumana Nawo Atithandiza Kudalira Yehova Nsanja ya Olonda, 4/15/2010
Matenda Akukhala Wamfupi Kwambiri
Matupi Aang’ono, Mitima Yabwino Nsanja ya Olonda, 2/15/2000
Matenda a Kuvutika Kudya
Zimene Achinyamata Amadzifunsa: Kodi Ndili Ndi Matenda Ovutika Kudya? Galamukani!, 10/2006
Kufuna Kuoneka Bwino Kuli M’poipira Pake Galamukani!, 9/8/2003
Matenda Akugwa
Zimene Muyenera Kudziwa Ponena za Matenda a Khunyu Galamukani!, 10/2013
Ndinafunitsitsa Kukwanitsa Cholinga Changa Galamukani!, 7/8/2005
Matenda Okomoka
Bwanji Ndimakomokakomoka? Galamukani!, 4/2007
Kutentha Thupi
Mwana Wanu Akatentha Thupi Galamukani!, 12/8/2003
Kusagwirizana ndi Chakudya
Kodi Kudana ndi Kusagwirizana ndi Zakudya kwa Thupi N’kosiyana Bwanji? Galamukani!, Na. 3 2016
Nyamakazi ya M’mafupa
Kodi Nyamakazi ya M’mafupa Imayamba Bwanji? Galamukani!, 8/2012
Chiseyeye
Zimene Mungachite Kuti Mupewe Chiseyeye Galamukani!, 6/2014
Mutu
Kodi Mungatani Ngati Mumadwala Mutu Waching’alang’ala? Galamukani!, 1/2011
Matenda Otupa Chiwindi
Matenda Otupa Chiwindi Amapha Mwakabisira Galamukani!, 8/2010
Matenda a Kuthamanga kwa Magazi
Kuteteza Ndiponso Kuletsa Matenda a Kuthamanga kwa Magazi Galamukani!, 5/8/2002
Matenda Otchedwa Huntington (HD)
Nthenda Yotchedwa Huntington—Tidziwe Bwino Tsoka Lachibadwa Limeneli Galamukani!, 4/8/2000
Chimfine
Tetezani Banja Lanu ku Matenda a Chimfine Galamukani!, 6/2010
Matenda Ofalitsidwa ndi Tizilombo
N’chifukwa Chiyani Ayambiranso?
Matenda a Kusowa Tulo
Onani Thanzi ➤ Kukhala ndi Thanzi Labwino ➤ Kugona
Matenda a M’chikodzodzo
Poizoni
Samalani ndi Poizoni Galamukani!, 12/2009
Vuto Lophunzira
Kuthandiza Ana Amene Ali ndi Vuto Lophunzira Galamukani!, 1/2009
Khate
Matenda Ofalitsidwa ndi Nthata Omwenso Amayambitsa Nyamakazi (Lyme Disease)
N’chifukwa Chiyani Ayambiranso? Galamukani!, 6/8/2003
Malungo
Kodi Mukudziwa Zotani pa Nkhani ya Malungo? Galamukani!, 7/2015
Matenda a Kusowa Zakudya M’thupi
Kodi Pagona Vutoli Mpati, Nanga Kuipa Kwake N’kotani?
“Mliri Wobisikawu” Utha Posachedwa!
Matenda Osiya Kusamba
Kupirira Mavuto Amene Azimayi Amakumana Nawo Akamasiya Kusamba Galamukani!, 11/2013
Matenda Oti Thupi Siligwirizana ndi Kuphatikiza Mankhwala Osiyanasiyana (MCS)
Kunenepa Kwambiri
Kodi Mungatani Kuti Mwana Wanu Asanenepe Kwambiri? Galamukani!, 3/2009
Kodi N’chiyani Chimachititsa Anthu Kunenepa Kwambiri?
Kodi Kunenepa Kwambiri Mungakuthetse Bwanji?
Kodi Kuchita Khama Kuti Muchepetse Kunenepa N’kwaphindudi?
Matenda Omwe Amachititsa Kuti Mafupa Akhale Ofewa Kwambiri (Osteogenesis Imperfecta)
Matendawa amatchedwanso, brittle bone
Kutumikira Mulungu Kuli Ngati Mankhwala Ake Nsanja ya Olonda, 11/15/2013
Ndikusangalala Ngakhale Kuti Ndine Wolumala Nsanja ya Olonda, 5/1/2009
Matenda Ofooketsa Mafupa (Osteoporosis)
Matenda Ofooketsa Mafupa Amayamba Mosaonekera Galamukani!, 6/2010
Kufa Ziwalo
Yehova Wandichitira Zazikulu Nsanja ya Olonda, 8/1/2015
Poliyo
Kusangalala Nawo “Moyo Uno” Nsanja ya Olonda, 6/1/2005
Vuto la Kusokonezeka Maganizo Pambuyo Pobereka
Ndinagonjetsa Vuto Langa Losokonezeka Maganizo Nditabereka Galamukani!, 8/8/2002
Matenda a Pulositeti
Zimene Mungachite Ngati Muli ndi Matenda a Pulositeti Galamukani!, 2/2011
Matenda Otchedwa Rett
Salankhula Koma Timamvana Galamukani!, 10/2008
Matenda a Scleroderma
“Ndimayesetsa Kuti Ndisamangoganizira za Matenda Anga” Galamukani!, 1/2015
Matenda Opindika Msana
Sanasiye Kutsatira Zimene Amakhulupirira Galamukani!, 8/2015
Vuto la Kudwala Chifukwa cha Kusintha kwa Nyengo (SAD)
Nyengo Imene Dzuwa Silituluka Galamukani!, 12/2008
Kudzivulaza
Kodi Achinyamata Amakumana ndi Mavuto Otani? (Bokosi: Achinyamata Akudzipweteka) Galamukani!, 9/2009
Zimene Achinyamata Amadzifunsa: Kodi Ndingatani Kuti Ndisiye Kudzivulaza? Galamukani!, 2/2006
Zimene Achinyamata Amadzifunsa: N’chifukwa Chiyani Ndimadzivulaza? Galamukani!, 1/2006
Matenda Olumala Msana
Yehova ‘Amanyamula Katundu Wanga Tsiku ndi Tsiku’ Nsanja ya Olonda, 8/15/2013
Kuvulala Msana
Yehova Anandithandiza pa Nthawi Yomwe Ndinkafunikiradi Kuthandizidwa Galamukani!, 11/2014
Zilonda za M’mimba
Banja Liyesedwa Chikhulupiriro Galamukani!, 5/8/2004
Matenda a Vitiligo
Matenda Osintha Mtundu wa Khungu Galamukani!, 10/8/2004
Kukhala Woyembekezera, Kubereka ndi Kusamalira Mwana
Abale a m’Komiti Yolankhulana ndi Achipatala angapereke kwa madokotala kabuku kokhala ndi njira zosiyanasiyana zochizira odwala popanda kuwaika magazi. Funsani akulu a mumpingo mwanu kuti mudziwe zambiri.
Zithunzi Zakale: Ignaz Semmelweis Galamukani!, Na. 3 2016
Zimene Mungachite Mwana Akabadwa Banja Losangalala, chigawo 6
Mwana Akamabadwa Pamachitika Zodabwitsa Galamukani!, 1/2011
Mayi Wathanzi Amaberekanso Mwana Wathanzi Galamukani!, 11/2009
Mmene Kumwa Mowa Mopitirira Muyeso Kumakhudzira Thanzi la Munthu Galamukani!, 10/8/2005
Njira Zatsopanozi Zabweretsanso Mavuto Atsopano
Mmene Mungatetezere Pathupi Panu Galamukani!, 1/8/2003
Ukalamba
Onaninso mutu wakuti Moyo Wachikhristu ➤ Kuthandiza Abale Athu ➤ Okalamba
Mungatani Kuti Muzisangalalabe Ngakhale Mutakalamba? Nsanja ya Olonda, 6/1/2015
N’chifukwa Chiyani Timakalamba? Galamukani!, 5/2006
Kukhala ndi Mphamvu Ngati Wachinyamata Mpaka Muyaya
Anthu Akuona Ukalamba Mosiyana ndi Kale Galamukani!, 9/8/2001
Kukalambirana Chinsinsi cha Banja, mutu 14
Kusamalira Odwala
Kodi Mungathandize Bwanji Mnzanu Kapena Wachibale Akadwala? Galamukani!, 10/2015
Khalanibe Olimba Mwauzimu Mukamasamalira Wachibale Amene Akudwala Nsanja ya Olonda, 5/15/2010
Madokotala Amakumana N’zambiri Galamukani!, 2/8/2005
Matenda Aakulu Ndi Nkhani ya Banja Lonse
Mmene Mabanja Amapiririra Matenda Aakulu
Pamene Wina M’banja Wadwala Chinsinsi cha Banja, mutu 10
Zizolowezi Zoipa
Onani mutu wakuti Dziko la Satana ➤ Zizolowezi Zoipa