Ndandanda za Upainiya Wothandiza
Zitsanzo za Mmene Mungakonzere Ndandanda ya Maola 15 a mu Utumiki Wakumunda Mlungu Uliwonse
Mmaŵa—Lolemba Mpaka Loŵeruka
Sande ingaloŵe pamalo pa tsiku lililonse
Tsiku Nthaŵi Maola
Lolemba Mmaŵa 2 1⁄2
Lachiŵiri Mmaŵa 2 1⁄2
Lachitatu Mmaŵa 2 1⁄2
Lachinayi Mmaŵa 2 1⁄2
Lachisanu Mmaŵa 2 1⁄2
Loŵeruka Mmaŵa 2 1⁄2
Maola Onse: 15
Masiku Aŵiri Athunthu
Masiku aŵiri alionse a mlungu angasankhidwe
Tsiku Nthaŵi Maola
Lachitatu Tsiku Lonse 7 1⁄2
Loŵeruka Tsiku Lonse 7 1⁄2
Maola Onse: 15
Madzulo Aŵiri ndi Kutha kwa Mlungu
Madzulo aŵiri alionse a mkati mwa mlungu angasankhidwe
Tsiku Nthaŵi Maola
Lolemba Madzulo 1 1⁄2
Lachitatu Madzulo 1 1⁄2
Loŵeruka Tsiku Lonse 8
Sande Theka la Tsiku 4
Maola Onse: 15
Masana a Mkati mwa Mlungu ndi Loŵeruka
Sande ingaloŵe pamalo pa tsiku lililonse
Tsiku Nthaŵi Maola
Lolemba Masana 2
Lachiŵiri Masana 2
Lachitatu Masana 2
Lachinayi Masana 2
Lachisanu Masana 2
Loŵeruka Tsiku Lonse 5
Maola Onse: 15
Ndandanda Yanga Yautumiki
Sankhani chiŵerengero cha maola a nthaŵi iliyonse
Tsiku Nthaŵi Maola
Lolemba
Lachiŵiri
Lachitatu
Lachinayi
Lachisanu
Loŵeruka
Sande
Maola Onse: 15