Ndandanda ya Mlungu wa April 19
MLUNGU WOYAMBIRA APRIL 19
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 1 Samueli 23-25
Na. 1: 1 Samueli 23:1-12
Na. 2: Kodi Tiyenera Kudziwa Chiyani pa Nkhani ya Isitala Ndiponso Kukondwerera Chaka Chatsopano (rs tsa. 242 ndime 4–tsa. 243 ndime 4)
Na. 3: N’chifukwa Chiyani Kupatsa Kuli Kopindulitsa? (Miy. 11:25)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 15: “Kodi Anthu Ena Angaphunzire Chiyani Poona Zochita Zanu?” Kambiranani mwa mafunso ndi mayankho.
Mph. 15: “Kodi Muli ndi Ufulu wa Kulankhula”? Nkhani yochokera mu Nsanja ya Olonda ya May 15, 2006, tsamba 13 mpaka 16. Tsindikani ubwino wolalikira molimba mtima.