Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 8/11 tsamba 2
  • Ndandanda ya Mlungu wa August 15

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa August 15
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2011
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA AUGUST 15
Utumiki Wathu wa Ufumu—2011
km 8/11 tsamba 2

Ndandanda ya Mlungu wa August 15

MLUNGU WOYAMBIRA AUGUST 15

Nyimbo Na. 10 ndi Pemphero

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

cf mutu 11, ndime 8-14 (Mph. 25)

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Masalimo 102–105 (Mph. 10)

Na. 1: Salimo 105:1-24 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: N’chifukwa Chiyani Sitiyenera Kulakalaka Zimene Tinkachita Kale Tisanayambe Kutumikira Yehova?—Luka 9:62 (Mph. 5)

Na. 3: Ufumu wa Mulungu Udzapezetsa Anthu onse Nyumba, Ntchito ndi Chitetezo—rs tsa. 378 ndime 6–tsa. 379 ndime 2 (Mph. 5)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 26

Mph. 5: Zilengezo.

Mph. 15: Thandizani Anthu Achidwi Kuti Apite Patsogolo. Nkhani yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 187 ndime 5 mpaka tsamba 188 ndime 3.

Mph. 15: “Muzilemba Malipoti Molondola N’kuwapereka Mwamsanga.” Mawu anu oyamba asafike mphindi imodzi, ndiyeno kambiranani mwa mafunso ndi mayankho pogwiritsa ntchito mafunso amene aperekedwa. Ikambidwe ndi woyang’anira utumiki.

Nyimbo Na. 47 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena