Ndandanda ya Mlungu wa March 19
MLUNGU WOYAMBIRA MARCH 19
Nyimbo Na. 58 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
bt mutu 3 ndime 12-18 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Yeremiya 8-11 (Mph. 10)
Na. 1: Yeremiya 10:17-25 ndi Yeremiya 11:1-5 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kukumbukira Imfa ya Yesu?—rs tsa. 70 ndime 3 mpaka tsa. 71 ndime 2 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Zizindikiro za pa Chikumbutso Zimaimira Chiyani?—rs tsa. 71 ndime 3 mpaka tsa. 72 ndime 1 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 15: Kodi Tikuphunzirapo Chiyani? Nkhani yokambirana. Werengani Mateyu 6:19-34. Kambiranani mmene mavesi amenewa angatithandizire mu utumiki.
Mph. 15: “Muzilalikira Molimba Mtima Kumalo a Ntchito ndi Amalonda.” Mafunso ndi mayankho. Funsani wofalitsa amene zinthu zimamuyendera bwino akamalalikira mu gawo la malonda.
Nyimbo Na. 108 ndi Pemphero