Ndandanda ya Mlungu wa September 17
MLUNGU WOYAMBIRA SEPTEMBER 17
Nyimbo Na. 131 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
bt mutu 12 ndime 9-13 ndi bokosi patsamba 97 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Ezekieli 46-48 (Mph. 10)
Na. 1: Ezekieli 48:1-14 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: N’chifukwa Chiyani Nthawi Zonse Tifunika Kuchita Zinthu Moona Mtima?—Aef. 4:25, 28; 5:1 (Mph. 5)
Na. 3: Mmene Mungayankhire Ngati Wina Atanena Kuti, ‘A Mboni za Yehova Muli Ndi Baibulo Lanulanu’—rs tsa. 330 ndime 1-4 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 30: “Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa—Kodi Ndidzachite Zotani Pamoyo Wanga? (Gawo 1)” Mafunso ndi mayankho. Gwiritsani ntchito mfundo zimene zili m’buku la Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri, tsamba 311 mpaka 317. Gwiritsani ntchito mawu opezeka m’ndime yoyamba ndi yomaliza monga mawu oyamba ndi omaliza pokambirana nkhaniyi.
Nyimbo Na. 88 ndi Pemphero