Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 7/15 tsamba 8
  • Zitsanzo za Ulaliki

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zitsanzo za Ulaliki
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Nkhani Yofanana
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2011
Onani Zambiri
Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
km 7/15 tsamba 8

Zitsanzo za Ulaliki

Nsanja ya Olonda August 1

“Tikucheza ndi anthu mwachidule n’kumakambirana nawo za vuto lomwe limagwera tonsefe. Inu mungandivomereze kuti munthu amene tinkamukonda akamwalira, zimakhala zowawa kwambiri. Koma taonani mawu olimbikitsa awa ochokera m’Baibulo. [Werengani Chivumbulutso 21:3, 4.] Baibulo limatithandiza kukhala ndi chiyembekezo choti abale athu amene anamwalira adzaukitsidwa. Magazini iyi ikufotokoza mmene zimenezi zidzachitikire.”

Galamukani! August

“Tikufuna kukusonyezani nkhani imene ikunena za kuchuluka kwa zinthu zomwe zimapezeka m’maselo a anthufe. [Asonyezeni chikuto cha Galamukani! ya August.] Anthu ena amakhulupirira kuti zinthu zamoyo zinachita kusintha kuchokera ku zinthu zina, pomwe ena amaona kuti pali winawake amene analenga zamoyo. Nanga inuyo maganizo anu ndi otani? [Yembekezerani ayankhe.] Magaziniyi ikufotokoza zomwe akatswiri apeza, zomwe zikusonyeza kuti maselo anapangidwa mogometsa. Zimenezi zachititsa asayansi ena kuyamba kuganiza kuti pali winawake amene analenga zinthu zamoyo.”

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena