Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 December tsamba 6
  • Muzitsanzira Mtumwi Paulo pa Nkhani Yolalikira Komanso Kuphunzitsa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzitsanzira Mtumwi Paulo pa Nkhani Yolalikira Komanso Kuphunzitsa
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Khalani ndi Luso Lothandiza Ena Kuona Mfundo Yofunika
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2005
  • Muzitsanzira Mariya Pokhala Odzichepetsa
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • ‘Chitani Zinthu Zonse Kaamba ka Uthenga Wabwino’
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2009
  • ‘Pitiriza Kudzipereka pa Kuphunzitsa’
    Nsanja ya Olonda—2010
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 December tsamba 6
Paulo akulalikira pamsika

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 17-18

Muzitsanzira Mtumwi Paulo pa Nkhani Yolalikira Komanso Kuphunzitsa

17:2, 3, 17, 22, 23

Kodi tingatsanzire bwanji Paulo?

  • Banja likulalikira pamsika

    Tizigwiritsa ntchito Malemba tikamakambirana ndi anthu komanso kumasintha ulaliki wathu kuti ugwirizane ndi anthu amene takumana nawo

  • Akulalikira mumsewu

    Tizilalikira kumalo komanso pa nthawi imene tingakumane ndi anthu ambiri

  • M’bale akulalikira munthu pogwiritsa ntchito Baibulo lake lomwe

    Tizichita zinthu mwaluso poyesetsa kudziwa zimene anthu amakhulupirira n’kugwiritsa ntchito zimenezo poyamba kukambirana nawo

FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi ndi kumalo komanso pa nthawi iti pamene ndingakumane ndi anthu ambiri m’gawo la mpingo wathu?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena