JANUARY 13-19
GENESIS 3-5
Nyimbo Na. 72 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mavuto Omwe Anabwera Chifukwa cha Bodza Loyamba”: (10 min.)
Gen. 3:1-5—Mdyerekezi ananenera Mulungu zabodza (w17.02 5 ¶9)
Gen. 3:6—Adamu ndi Hava sanamvere Mulungu (w00 11/15 25-26)
Gen. 3:15-19—Mulungu anawapatsa chilango (w12 9/1 4 ¶2; w04 1/1 29 ¶2; it-2 186)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Gen. 4:23, 24—N’chifukwa chiyani Lameki anapeka ndakatuloyi? (it-2 192 ¶5)
Gen. 4:26—Kodi anthu a m’nthawi ya Inosi anayamba “kuitanira pa dzina la Yehova” m’njira yotani? (it-1 338 ¶2)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Gen. 4:17–5:8 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: N’chiyani chakusangalatsani ndi mmene wofalitsayu anayambira kukambirana ndi mwininyumba? Kodi tikuphunzirapo chiyani pa zimene ofalitsawa achita pokonza zoti adzapange ulendo wobwereza?
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 3)
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako musiyireni magazini yatsopano yomwe ili ndi nkhani imene mwininyumba anatchula. (th phunziro 2)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kodi Tingayambe Bwanji Kukambirana ndi Anthu Pogwiritsa Ntchito Timapepala?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuonera vidiyo yomwe ikusonyeza zimene tingachite kuti tiyambe kukambirana ndi anthu pogwiritsa ntchito timapepala. Kenako kambiranani zimene mukuphunzirapo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 68
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 70 ndi Pemphero