Zimene Zili M’magaziniyi
M’MAGAZINIYI MULI
Nkhani Yophunzira 44: January 5-11, 2026
2 Zimene Mungachite Kuti Muzisangalalabe Ngakhale Kuti Ndinu Achikulire
8 Kodi Ndisiye Kuyendetsa Galimoto?
Nkhani Yophunzira 45: January 12-18, 2026
10 Zimene Mungachite Kuti Muzisangalalabe Mukamasamalira Wachibale Amene Akudwala Kapena Achikulire
Nkhani Yophunzira 46: January 19-25, 2026
16 Muziganizira za Yesu Yemwe ndi Mkulu wa Ansembe Amene Amatimvera Chisoni
Nkhani Yophunzira 47: January 26, 2026–February 1, 2026
22 “Ndiwe Munthu Wokondedwa Kwambiri”!
28 “Muziyesetsa ndi Mtima Wonse Kusunga Umodzi Umene Timaupeza Mothandizidwa ndi Mzimu Woyera”
30 Zimene Zingathandize Akazi Omwe Akuchitiridwa Nkhanza
31 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
32 Mawu a M’Baibulo—Muzigwiritsa Ntchito ‘Mphatso Yanu ya Uzimu’