November Magazini Yophunzira Zimene Zili M’magaziniyi NKHANI YOPHUNZIRA 44 Zimene Mungachite Kuti Muzisangalalabe Ngakhale Kuti Ndinu Achikulire Kodi Ndisiye Kuyendetsa Galimoto? NKHANI YOPHUNZIRA 45 Zimene Mungachite Kuti Muzisangalalabe Mukamasamalira Wachibale Amene Akudwala Kapena Wachikulire NKHANI YOPHUNZIRA 46 Tiziganizira za Yesu Amene Ndi Mkulu wa Ansembe Wathu Yemwe Amatimvera Chisoni NKHANI YOPHUNZIRA 47 “Ndiwe Munthu Wokondedwa Kwambiri” “Muziyesetsa ndi Mtima Wonse Kusunga Umodzi Umene Timaupeza Mothandizidwa ndi Mzimu Woyera” Zimene Zingathandize Akazi Omwe Akuchitiridwa Nkhanza Mafunso Ochokera kwa Owerenga MAWU A M’BAIBULO Muzigwiritsa Ntchito ‘Mphatso Yanu ya Uzimu’