Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • ijwbq nkhani 7
  • Kodi Mulungu Ndi Mphamvu Yosaoneka?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mulungu Ndi Mphamvu Yosaoneka?
  • Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Yankho la m’Baibulo
  • Magwero Oposa Munthu a Mzumu Woyera
    Mzimu Woyera—Mphamvu Yochirikiza Dongosolo Latsopano Likudza’lo!
  • Mphamvu za Mulungu Zimaonekera mu Nyenyezi
    Nsanja ya Olonda—2008
  • Kupeza Gwero la Mphamvu Zonse
    Galamukani!—2005
  • Kodi Yehova Ndani?
    Nsanja ya Olonda—1998
Onani Zambiri
Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
ijwbq nkhani 7
Munthu akuyang’ana nyenyezi

Mulungu / Kodi Mulungu Ndi Mphamvu Yosaoneka?

Yankho la m’Baibulo

Mulungu amasonyeza mphamvu zake zopanda malire m’chilengedwe chonse. Ponena za nyenyezi mabiliyoni osawerengeka zimene analenga, Baibulo limati: “Kwezani maso anu kumwamba muone. Kodi ndani amene analenga zinthu zimenezo? Ndi [Mulungu] amene akutsogolera gulu lonse la nyenyezizo malinga ndi chiwerengero chake, ndipo amaziitana potchula iliyonse dzina lake. Chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake zoopsa, ndiponso chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zambiri zochitira zinthu, palibe imene imasowa.”—Yesaya 40:25, 26.

Koma Mulungu alinso ndi makhalidwe ena kuwonjezera pa mphamvu. Baibulo limasonyeza kuti iye amatha kukonda kapena kudana ndi zinthu zinazake. (Salimo 11:5; Yohane 3:16) Baibulo limasonyezanso kuti Mulungu amakhudzidwa ndi zimene anthu amachita.—Salimo 78:40, 41.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena