Zamkatimu
April 2009
Mungatani Ngati Mumapanikizika ndi Sukulu Ndiponso Zinthu Zina?
N’chifukwa chiyani ana ambiri amapanikizika ndi sukulu? Kodi makolo ndi aphunzitsi angachite chiyani kuti awathandize?
3 Ophunzira Ambiri Amapanikizika ndi Sukulu
9 Kodi Makolo Mungathandize Bwanji Ana Anu?
11 Mzinda wa Bucharest Ndi Wochititsa Chidwi
16 Zimatheka Bwanji Kuphunzitsa Njovu?
19 Munthu Woyamba Kujambula Mapu a Dziko Lonse
Kodi Kukachitika Ngozi Mumadziwitsa Ndani? 12
Kodi maphunziro a anthu othandiza anzawo pangozi amakhala otani? Kodi iwo amathandiza bwanji pakachitika ngozi? Werengani zimene munthu wina wogwira ntchito imeneyi ku Canada anafotokoza.
Kodi Kukhulupirika M’banja N’kutani? 28
Kodi kusirira mkazi kapena mwamuna wina n’koipa? Kodi mungapewe bwanji moyo wosakhulupirika m’banja?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Taken by courtesy of City of Toronto EMS