Lamlungu
“Limba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu. Yembekezera Yehova”—SALIMO 27:14
M’MAWA
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
9:30 Nyimbo Na. 73 ndi Pemphero
9:40 NKHANI YOSIYIRANA: Kutsogoloku Tidzafunika Kulimba Mtima
Akadzalengeza Kuti “Bata ndi Mtendere!” (1 Atesalonika 5:2, 3)
Babulo Wamkulu Akamadzawonongedwa (Chivumbulutso 17:16, 17)
Polengeza Uthenga Wokhala Ngati Matalala (Chivumbulutso 16:21)
Gogi wa Kudziko la Magogi Akamadzaukira Anthu a Mulungu (Ezekieli 38:10-12, 14-16)
Pa Aramagedo (Chivumbulutso 16:14, 16)
Pokonzanso Dziko Lapansili (Yesaya 65:21)
Pa Mayesero Omaliza (Chivumbulutso 20:3, 7, 8)
11:10 Nyimbo Na. 8 ndi Zilengezo
11:20 NKHANI YA ONSE: Kodi Chiyembekezo Chakuti Akufa Adzauka Chimatithandiza Bwanji Kukhala Olimba Mtima? (Maliko 5:35-42; Luka 12:4, 5; Yohane 5:28, 29; 11:11-14)
11:50 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
12:20 Nyimbo Na. 151 ndi Kupuma
MASANA
1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
1:45 Nyimbo Na. 5
1:50 VIDIYO: Nkhani ya Yona—Yophunzitsa Kulimba Mtima Komanso Chifundo (Yona 1-4)
2:40 Nyimbo Na. 71 ndi Zilengezo
2:50 Amene Ali Kumbali Yathu ndi Ambiri Kuposa Amene Akutitsutsa (Deuteronomo 7:17, 21; 28:2; 2 Mafumu 6:16; 2 Mbiri 14:9-11; 32:7, 8, 21; Yesaya 41:10-13)
3:50 Nyimbo Yomaliza Komanso Pemphero