Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 3/06 tsamba 3
  • Zofunika Kukumbukira pa Chikumbutso

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zofunika Kukumbukira pa Chikumbutso
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2006
  • Nkhani Yofanana
  • Zofunika Kukumbukira pa Chikumbutso
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2007
  • Zofunika Kukumbukira pa Chikumbutso
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2004
  • Zofunika Kukumbukira pa Chikumbutso
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2005
  • Zofunika Kukumbukira pa Chikumbutso
    Utumiki wathu wa Ufumu—2002
Onani Zambiri
Utumiki Wathu wa Ufumu—2006
km 3/06 tsamba 3

Zofunika Kukumbukira pa Chikumbutso

Chikumbutso cha chaka chino chidzachitika Lachitatu, pa April 12. Akulu akumbukire zinthu izi:

◼ Pokonza nthawi ya mwambowu, onetsetsani kuti musapereke zizindikiro dzuwa lisanalowe.

◼ Aliyense, ngakhale wokamba nkhani, auzidwe nthawi yeniyeni ndi kumene kudzachitikire mwambowu.

◼ Mupezeretu mkate ndi vinyo woyenera.—Onani Nsanja ya Olonda ya February 15, 2003, tsamba 14 ndi 15.

◼ Mbale, matambula, tebulo labwino ndi nsalu za patebulo ziyenera kubwera ku holo nthawi yabwino n’kuziikiratu pamalo ake.

◼ Nyumba ya Ufumu kapena malo ena alionse ochitirapo mwambowu akonzedweretu bwinobwino.

◼ Muyenera kusankhiratu akalinde ndi operekera zizindikiro ndipo muwauziretu ntchito yawo ndi mmene adzayendetsere zinthu, ndiponso kuti afunika adzavale zovala zaulemu ndiponso kudzikonza bwino.

◼ Konzani zokapereka zizindikirozo kwa wodzozedwa aliyense amene akudwala ndipo satha kupezekapo.

◼ Ngati mipingo ingapo idzagwiritsa ntchito Nyumba ya Ufumu imodzi, mipingoyo iyenera kugwirizana bwino, kuti anthu asadzapanikizane pakhonde, pakhomo, m’tinjira, ndi koimika magalimoto.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena