Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 April tsamba 1
  • Zitsanzo za Ulaliki

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zitsanzo za Ulaliki
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • GALAMUKANI!
  • GALAMUKANI!
  • Baibulo Limaphunzitsa Chiyani
  • LEMBANI ULALIKI WANUWANU
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 April tsamba 1
Anthu amene anapezeka pa Msonkhano wa Mayiko wa Mboni za Yehova ku New Jersey, U.S.A., mu 2014

Abale ndi alongo pamsonkhano wa mayiko mu 2014, ku New Jersey, U.S.A.

Zitsanzo za Ulaliki

GALAMUKANI!

Magazini ya Galamukani! Na. 2 2016 | Kodi Baibulo Langokhala Buku Labwino Basi?

Perekani Magaziniyo: Ndikufuna ndikupatseni magazini yatsopano iyi ya Galamukani!

Funso: Taonani funso lomwe lili patsamba 2. Kodi inuyo mukuganiza bwanji?

Lemba: Luka 7:35

Nkhani imeneyi ikufotokoza mmene tingapindulire ndi mfundo za m’Baibulo.

GALAMUKANI!

Funso: Kodi nanunso mumaona kuti kutsatira mfundo ya palemba ili n’kothandiza?

Lemba: Mat. 6:34

Perekani Magaziniyo: [Tsegulani nkhani yakuti, “Zimene Baibulo Limanena—Nkhawa.”] Nkhaniyi ikufotokoza mmene Baibulo lingatithandizire tikakhala ndi nkhawa.

Baibulo Limaphunzitsa Chiyani

Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

Funso: Anthu ambiri amene amakhulupirira Mulungu, amafunitsitsa kumudziwa bwino. Kodi mukudziwa kuti Baibulo limatilimbikitsa kuti tiyandikire Mulungu?

Lemba: Yak. 4:8a

Perekani Bukulo: Buku ili linalembedwa n’cholinga chotithandiza kuphunzira za Mulungu pogwiritsa ntchito Baibulo. [Sonyezani mutu woyamba wa buku la Baibulo Limaphunzitsa Chiyani.]

LEMBANI ULALIKI WANUWANU

Potengera zitsanzozi, konzani njira imene mungagwiritse ntchito.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena