Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 May tsamba 1
  • Zitsanzo za Ulaliki

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zitsanzo za Ulaliki
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • NSANJA YA OLONDA
  • NSANJA YA OLONDA (tsamba lomaliza)
  • BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI
  • LEMBANI NJIRA INA IMENE MUNGAGWIRITSE NTCHITO
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 May tsamba 1
Mwamuna ndi mkazi wake akuphunzira pogwiritsa ntchito tabuleti

Banja likuphunzira Baibulo pogwiritsa ntchito tabuleti

Zitsanzo za Ulaliki

NSANJA YA OLONDA

Nsanja ya Olonda Na. 3 2016 | Kodi Mungatani Munthu Yemwe Munkamukonda Akamwalira

Funso: Kodi inuyo mumaona kuti mawu awa adzakwaniritsidwadi?

Lemba: Chiv. 21:3, 4

Perekani Magaziniyo: Magazini iyi ikufotokoza mmene Mulungu adzakwaniritsire mawu amenewa komanso mmene moyo udzakhalire mawuwa akadzakwaniritsidwa.

NSANJA YA OLONDA (tsamba lomaliza)

Funso: Taonani funso ili. [Musonyezeni funso loyamba patsamba 16 komanso zimene anthu ena amayankha.] Kodi inuyo mukuganiza bwanji?

Lemba: Sal. 83:18

Perekani Magaziniyo: Nkhaniyi ikufotokoza zimene Baibulo limanena zokhudza dzina la Mulungu.

BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI

Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

Funso: Anthu ena amaganiza kuti Mulungu ndi amene akulamulira dzikoli. Koma kodi mukudziwa kuti zimenezi n’zosemphana ndi zimene Baibulo limaphunzitsa?

Lemba: 1 Yoh. 5:19

Perekani Bukulo: Bukuli likufotokoza momveka bwino zimene Baibulo limanena pa nkhaniyi ndi zinanso zambiri.

LEMBANI NJIRA INA IMENE MUNGAGWIRITSE NTCHITO

Potengera zitsanzozi, konzani njira imene mungagwiritse ntchito.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena