Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 March tsamba 1
  • Zitsanzo za Ulaliki

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zitsanzo za Ulaliki
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • NSANJA YA OLONDA
  • KODI UFUMU WA MULUNGU N’CHIYANI?
  • KAPEPALA KOITANIRA ANTHU KU CHIKUMBUTSO
  • LEMBANI ULALIKI WANUWANU
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 March tsamba 1
A Mboni za Yehova a ku Albania akupatsa munthu kapepala koitanira anthu ku Chikumbutso

Akuitanira anthu ku Chikumbutso ku Albania

Zitsanzo za Ulaliki

NSANJA YA OLONDA

Nsanja ya Olonda Na. 2 2017 | Kodi Mulandira Mphatso Yaikulu Imene Mulungu Wapereka?

Funso: Kodi mukuona kuti mphatso yaikulu kwambiri imene Mulungu anatipatsa ndi iti?

Lemba: Yoh. 3:16

Perekani Magaziniyo: Nsanja ya Olonda iyi ikufotokoza chifukwa chimene Mulungu anatumizira Yesu padziko lapansi kuti adzatifere komanso mmene tingasonyezere kuti timayamikira mphatsoyi.

KODI UFUMU WA MULUNGU N’CHIYANI?

Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani?

Funso: [Musonyezeni tsamba loyamba la kapepalako.] Kodi mungayankhe bwanji funso ili? Kodi Ufumu wa Mulungu ndi chinachake chimene chimakhala mumtima mwa munthu aliyense, mawu ongophiphiritsira kapena ndi boma limene lili kumwamba?

Lemba: Dan. 2:44; Yes. 9:6

Perekani Kapepalako: Kapepala aka kakufotokoza zimene Ufumu wa Mulungu ungakuchitireni.

KAPEPALA KOITANIRA ANTHU KU CHIKUMBUTSO

2017 Kapepala koitanira anthu ku Chikumbutso

Tikuitanira anthu ku mwambo wofunika kwambiri. [Perekani kapepalako.] Pa 11 April, anthu mamiliyoni ambiri padziko lonse adzasonkhana kuti akumbukire imfa ya Yesu ndiponso kumvetsera nkhani ya m’Baibulo yokhudza mmene imfayi ingatithandizire. Kapepalaka kakusonyeza nthawi ndiponso malo amene mwambowu udzachitikire kunoko. Tidzasangalala kwambiri ngati mutabwera.

LEMBANI ULALIKI WANUWANU

Potengera zitsanzozi, konzani njira imene mungagwiritse ntchito

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena