Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 March tsamba 1
  • Zitsanzo za Ulaliki

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zitsanzo za Ulaliki
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • NSANJA YA OLONDA
  • NSANJA YA OLONDA (tsamba lomaliza)
  • KAPEPALA KOITANIRA ANTHU KU CHIKUMBUTSO
  • LEMBANI ULALIKI WANUWANU
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 March tsamba 1
Kuchita Mwambo Wokumbukira Imfa ya Khristu

Anthu ali pamwambo wokumbukira imfa ya Khristu ku Germany

Zitsanzo za Ulaliki

NSANJA YA OLONDA

Magazini ya Nsanja ya Olonda, Na. 2 2016 | N’chifukwa Chiyani Yesu Anavutika Mpaka Kufa?

Funso: Kodi mumadziwa zimene lemba ili limanena?

Lemba: Yoh. 3:16

Perekani Magaziniyo: Magaziniyi ikufotokoza mwayi umene tili nawo chifukwa choti Yesu analolera kuvutika mpaka kufa.

NSANJA YA OLONDA (tsamba lomaliza)

Funso: Taonani funso ili komanso zimene anthu ena amayankha. [Werengani funso loyamba ndi mayankho ake.] Kodi inuyo mungayankhe bwanji?

Lemba: Mat. 4:1-4

Perekani Magaziniyo: Zimenezi zikusonyeza kuti Mdyerekezi alikodi ndipo si mphamvu chabe ya zinthu zoipa, chifukwa ankayankhulana ndi Yesu n’kumamuyesa. Kodi ndi zinthu zinanso ziti zimene Baibulo limanena zokhudza Mdyerekezi? Werengani nkhaniyi kuti mumve zambiri.

KAPEPALA KOITANIRA ANTHU KU CHIKUMBUTSO

Kapepala koitanira anthu ku chikumbutso cha imfa ya Khristu mu 2016

Perekani Kapepalako: Tikugawira anthu kapepala aka kowaitanira kumwambo wofunika kwambiri. [Apatseni kapepalako.] Pa 23 March, anthu ambiri padziko lonse adzasonkhana pamwambo wokumbukira imfa ya Yesu Khristu. Kudzakhala nkhani ya m’Baibulo yofotokoza mwayi umene tili nawo chifukwa cha imfa ya Yesu ndipo simudzafunikira kulipira kalikonse. Kapepalaka kakusonyeza nthawi ndi malo amene mwambowu udzachitikire kwathu kuno. Mudzayesetse kubwera.

LEMBANI ULALIKI WANUWANU

Potengera zitsanzozi, konzani njira imene mungagwiritse ntchito.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena