Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 January tsamba 5
  • Musamade Nkhawa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Musamade Nkhawa
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mukukumbukira?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
  • ‘Mukhale Okhutira Ndi Zimene Muli Nazo Panopa’
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Mukhoza Kutumikira Yehova Ngakhale Makolo Anu Si Chitsanzo Chabwino
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Muzisonyeza Chikondi Chokhulupirika
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 January tsamba 5

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

Musamade Nkhawa

Mbalame; maluwa

Pa ulaliki wake wapaphiri, Yesu anati: “Lekani kudera nkhawa moyo wanu.” (Mat. 6:25) Mwachibadwa, anthu ochimwafe timakonda kuda nkhawa. Kuwonjezera pamenepo, m’dziko la Satanali timakumana ndi zinthu zambiri zodetsa nkhawa. Komabe Yesu anaphunzitsa otsatira ake kuti ayenera kupewa kuda nkhawa kwambiri. (Sal. 13:2) Ananena zimenezi chifukwa ankadziwa kuti kudera nkhawa ngakhale pa zofunika zatsiku ndi tsiku, kungatisokoneze komanso kungapangitse kuti tizilephera kuika zinthu zokhudza Ufumu pamalo oyamba. (Mat. 6:33) Pali mfundo zinanso zimene Yesu anatchula zomwe zingatithandize kuti tisamadere nkhawa zinthu zosafunika kwenikweni.

  • Mat. 6:26​—Kodi tingaphunzire chiyani kuchokera kwa mbalame? (w16.07 9-10 ¶11-13)

  • Mat. 6:27​—N’chifukwa chiyani tinganene kuti kuda nkhawa kumangowonongetsa nthawi komanso mphamvu? (w05 11/1 22 ¶5)

  • Mat. 6:28-30​—Kodi tingaphunzire chiyani kuchokera ku maluwa akutchire? (w16.07 10-11 ¶15-16)

  • Mat. 6:31, 32​—Kodi Akhristu amasiyana bwanji ndi anthu ena? (w16.07 11 ¶17)

Kodi ndi zinthu ziti zimene ndikufuna ndisiye kuzidera nkhawa?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena