Mkulu wa ansembe akulowa m’Malo Oyera Koposa
Zimene Tinganene
●○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi Mulungu amawaona bwanji anthu amene amafunitsitsa kumudziwa?
Lemba: 1Pe 5:6, 7
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Mulungu amatiganiziradi aliyense payekha?
○● ULENDO WOBWEREZA
Funso: Kodi Mulungu amatiganiziradi aliyense payekha?
Lemba: Mt 10:29-31
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi tikudziwa bwanji kuti Mulungu amatimvetsa?