Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsamba 16
  • Kodi Mudzachita Upainiya Wothandiza M’mwezi wa March Kapena April?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mudzachita Upainiya Wothandiza M’mwezi wa March Kapena April?
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Konzekerani Panopo Kuwonjezera Utumiki Wanu
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2012
  • Mwayi Winanso Wotamanda Yehova
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Apainiya Othandiza 3,000 Akufunika
    Utumiki Wathu wa Ufumu—1997
  • Lengezani Ulemerero wa Yehova
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2007
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 January tsamba 16
Ofalitsa akutuluka m’Nyumba ya Ufumu ali ndi kashelefu kamatayala.

“Chikondi chimene Khristu ali nacho chimatikakamiza.”​—2Ak 5:14

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kodi Mudzachita Upainiya Wothandiza M’mwezi wa March Kapena April?

Kodi mungakonde kudzachita zambiri mu utumiki pa nyengo ya Chikumbutso? (2Ak 5:​14, 15) Pa miyezi ya March ndi April amene adzachite upainiya wothandiza adzatha kusankha kupereka maola 30 kapena 50. Ngati mungakwanitse kudzachita utumikiwu pa miyezi imeneyi, lembani fomu n’kuipereka ku Komiti ya Utumiki ya Mpingo. Mwezi uliwonse, mayina a anthu amene avomerezedwa kuchita upainiya wothandiza adzalengezedwa. Zimenezi zidzachititsa kuti anthu ena mumpingo azithandiza apainiyawa polowa nawo mu utumiki. Tiyeni tonse tidzagwiritse ntchito nthawi ya Chikumbutsoyi kuti tidzalimbikitsane komanso kuwonjezera luso lathu lolalikira.​—1At 5:11.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena