Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsamba 12
  • Zinthu Zimatiyendera Bwino Tikamatsatira Malangizo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zinthu Zimatiyendera Bwino Tikamatsatira Malangizo
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Zinyama?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Malangizo Achikondi a Bambo Opita kwa Mwana Wake
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • ‘Kodi Munthu Angakhale Waphindu kwa Mulungu?’
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kodi Likasa la Pangano N’chiyani?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 January tsamba 12
Mfumu Davide limodzi ndi Aisiraeli ena akuimba komanso kuvina pamene Alevi anyamula likasa la pangano.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zinthu Zimatiyendera Bwino Tikamatsatira Malangizo

Davide ankafuna kuti likasa la pangano libwerere ku Yerusalemu (1Mb 13:3)

Pa ulendo woyamba zinakanika atalola kuti likasalo linyamulidwe m’njira yosayenera (1Mb 15:13; w03 5/1 10-11)

Davide atafufuza malangizo a Yehova, zinthu zinamuyendera bwino (1Mb 15:2; 16:11; w03 5/1 11 ¶13)

Yehova amayamikira tikamachita zinthu ndi zolinga zabwino. Komabe, kuti azisangalala ndi zochita zathu tiyenera kumatsatira malangizo ake.​—De 30:16.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena