Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsamba 13
  • Muzikhalabe Wosangalala Ngakhale Pamene Zinthu Sizikuyenda Bwino

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzikhalabe Wosangalala Ngakhale Pamene Zinthu Sizikuyenda Bwino
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mukukumbukira?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2021
  • Muzikhala Wofunitsitsa Kuchita Zimene Mulungu Amafuna
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Muzithandiza Achinyamata Kuti Azichita Zambiri
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kodi Mumagwira Ntchito Zonyozeka?
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 January tsamba 13

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzikhalabe Wosangalala Ngakhale Pamene Zinthu Sizikuyenda Bwino

Davide ankafunitsitsa kumangira Yehova kachisi wokongola (1Mb 17:1, 2; w06 7/15 19 ¶1)

Yehova anauza Davide kuti iye si amene adzamange kachisiyo (1Mb 17:4)

Davide sanafooke koma anapitirizabe kugwira ntchito imene Yehova anam’patsa (1Mb 17:7; 18:14)

Zithunzi: 1. M’bale yemwe akuoneka wokhumudwa wakhala panjinga ya anthu olumala ndipo akupuma pogwiritsa ntchito okosijeni. 2. M’bale uja akusangalala pamene akulalikira pogwiritsa ntchito kashelefu.

Ngati simungakwanitse kuchita utumiki winawake chifukwa cha msinkhu, thanzi kapena zinthu zina, musamafooke koma muzingochita zimene mungakwanitse kuchitazo.​—Mac 18:5; w21.08 22-23 ¶11.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena