Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsamba 9
  • Yehova ndi “Tate wa Ana Amasiye”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova ndi “Tate wa Ana Amasiye”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Zosankha Zomwe Zimasonyeza Kuti Timadalira Yehova
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Muzigwiritsa Ntchito Mfundo za M’Baibulo Pothandiza Ana Anu Kuti Zinthu Ziwayendere Bwino
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • “Sankhani . . . Amene Mukufuna Kum’tumikira”
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2025
  • Tizivomereza Modzichepetsa Kuti Sitikudziwa Zonse
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2025
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 May tsamba 9
M’bale wachinyamata yemwe ali mu nkhani yakuti “Mukhoza Kutumikira Yehova Ngakhale Makolo Anu Si Chitsanzo Chabwino” akulankhulana ndi m’bale wina wolimba mwauzimu pamene ali limodzi mu utumiki.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Yehova ndi “Tate wa Ana Amasiye”

Chaka chilichonse, achinyamata ambiri amasankha kukhala mabwenzi a Yehova. (Sl 110:3) Yehova amakukondani kwambiri. Iye amadziwa bwino mavuto amene aliyense payekha akukumana nawo ndipo analonjeza kuti adzakuthandizani kuti muzikwanitsa kumutumikira. Ngati mukuleredwa m’banja la kholo limodzi, muzikumbukira kuti Yehova ndi “tate wa ana amasiye.” (Sl 68:5) Yehova angakuthandizeni kuti zinthu zizikuyenderani bwino posatengera zimene mukukumana nazo kunyumba kwanu.​—1Pe 5:10.

Chithunzi cha muvidiyo yakuti “Anthu Omwe Apambana pa Nkhondo Yachikhulupiriro​—Amene Akuleredwa Ndi Kholo Limodzi.” Tammy Ludlow.

ONERANI VIDIYO YAKUTI ANTHU OMWE APAMBANA PA NKHONDO YACHIKHULUPIRIRO​—AMENE AKULEREDWA NDI KHOLO LIMODZI, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Kodi tikuphunzira chiyani pa zitsanzo za Tammy, Charles ndi Jimmy

  • Kodi ndi lonjezo liti lopezeka pa Salimo 27:10, lomwe lingalimbikitse achinyamata amene akuleredwa ndi kholo limodzi?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena