Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 November tsamba 4
  • Musamatsanzire Elifazi Potonthoza Ena

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Musamatsanzire Elifazi Potonthoza Ena
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Pewani Maganizo Olakwika
    Nsanja ya Olonda—2005
  • Yobu Afupidwa Chifukwa Chokhulupirika
    Nsanja ya Olonda—1998
  • Yehova Amasangalala Tikamapempherera Ena
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Tizilimbikitsa Anzathu Powayankhula Mokoma Mtima
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 November tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Musamatsanzire Elifazi Potonthoza Ena

Elifazi anauza Yobu kuti anthu sangasangalatse Mulungu (Yob 15:​14-16; w05 9/15 26 ¶4-5)

Elifazi anasonyeza kuti Yobu anali woipa ndipo n’chifukwa chake ankakumana ndi mavuto (Yob 15:20)

Mawu amene Elifazi analankhula sanatonthoze Yobu (Yob 16:​1, 2)

Elifazi akuloza Yobu amene ali ndi zilonda thupi lonse ndipo anzake ena awiri amene akunamizira kudzamutonthoza akuonerera.

Zomwe Elifazi anauza Yobu zinali zabodza. Yehova amatiyamikira kwambiri chifukwa cha khama lomwe timasonyeza pomutumikira. (Sl 149:4) Ngakhale anthu olungama amadziwa kuti azikumana ndi mavuto.—Sl 34:19.

FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi ndingatani kuti ‘ndizilankhula molimbikitsa kwa amtima wachisoni’?—1At 5:14; w15 2/15 9 ¶16.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena