Mawu Oyamba
Kodi mungatani kuti mukhale ndi tsogolo labwino? M’magaziniyi muona zinthu zosiyanasiyana zimene anthu ena amachita pofuna kukhala ndi tsogolo labwino. Muonanso kumene mungapeze malangizo odalirika omwe angakuthandizeni kuti mukhaledi ndi tsogolo labwino.