Tito 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 (osati chifukwa cha ntchito zolungama zimene tinachita,+ koma chifukwa cha chifundo chake),+ anatipulumutsa potisambitsa kuti tifike ku moyo watsopano.+ Komanso anatipulumutsa potithandiza ndi mzimu woyera kuti tikhale atsopano.+ Tito Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:5 Nsanja ya Olonda,10/15/2008, tsa. 304/15/2004, tsa. 127/15/1991, tsa. 12
5 (osati chifukwa cha ntchito zolungama zimene tinachita,+ koma chifukwa cha chifundo chake),+ anatipulumutsa potisambitsa kuti tifike ku moyo watsopano.+ Komanso anatipulumutsa potithandiza ndi mzimu woyera kuti tikhale atsopano.+