Ekisodo 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Utenge mafuta+ onse okuta matumbo,+ mafuta a pachiwindi,*+ impso ziwiri ndi mafuta ake, n’kuzitentha* paguwa lansembe.+
13 Utenge mafuta+ onse okuta matumbo,+ mafuta a pachiwindi,*+ impso ziwiri ndi mafuta ake, n’kuzitentha* paguwa lansembe.+