Salimo 127:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 127 Yehova akapanda kumanga nyumba,+Omanga nyumbayo amagwira ntchito pachabe.+Yehova akapanda kulondera mzinda,+Alonda amakhala maso pachabe.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 127:1 Nsanja ya Olonda,12/1/1993, tsa. 3210/1/1989, ptsa. 27-29
127 Yehova akapanda kumanga nyumba,+Omanga nyumbayo amagwira ntchito pachabe.+Yehova akapanda kulondera mzinda,+Alonda amakhala maso pachabe.+