5 Udzafa mu mtendere.+ Anthu adzakufukizira zinthu zonunkhira+ ngati mmene anachitira ndi makolo ako, mafumu amene analipo iwe usanabadwe.+ Polira maliro ako adzanena kuti,+ ‘Kalanga ine mbuyanga!’+ pakuti ‘Ine ndalankhula mawu amenewa,’ watero Yehova.”’”’”